Ezekieli 23:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

omangira malamba m'cuuno mwao, ndi nduwira zazikuru zonika pamitu pao, maonekedwe ao ngati akalonga onsewo, akunga a ku Babulo, dziko la kubadwa kwao ndi Kasidi.

Ezekieli 23

Ezekieli 23:10-17