Ezekieli 23:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anaumirira Aasuri, ziwanga, ndi akazembe oyandikizana naye, obvala zangwiro, anthu oyenda pa akavalo, onsewo anyamata ofunika.

Ezekieli 23

Ezekieli 23:6-14