Ezekieli 23:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwowa anabvula umarisece wace, anatenga ana ace amuna ndi akazi, namupha iyeyu ndi lupanga; ndi dzina lace linamveka mwa akazi atamcitira maweruzo.

Ezekieli 23

Ezekieli 23:7-13