Ezekieli 23:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, Wobadwa ndi munthu iwe, panali akazi awiri, mai wao ndi mmodzi;