Ezekieli 22:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu a m'dziko anazunzazunza, nalandalanda mwaciwawa, napsinja ozunzika ndi aumphawi, nazunza mlendo wopanda cifukwa.

Ezekieli 22

Ezekieli 22:20-31