Ezekieli 22:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pali ciwembu ca aneneri ace pakati pace, ngati mkango wobangula womwetula nyama, analusira miyoyo, alanda cuma ndi za mtengo wace, acurukitsa amasiye pakati pace.

Ezekieli 22

Ezekieli 22:15-29