Ezekieli 21:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakutsanulira mkwiyo wanga, ndidzakuuzira ndi moto wa kuzaza kwanga, ndidzakuperekanso m'manja mwa anthu ankharwe odziwa kuononga.

Ezekieli 21

Ezekieli 21:29-32