Ezekieli 21:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uiike njira yodzera lupanga kumka ku Raba wa ana a Amoni, ndi ya ku Yuda ku Yerusalemu, mudzi walinga.

Ezekieli 21

Ezekieli 21:17-25