Ezekieli 21:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndalozetsa nsonga ya lupanga ku zipata zao zonse, kuti mtima wao usungunuke, ndi kukhumudwa kwao kucuruke; ha! analituula linyezimire, analisongoza liphe,

Ezekieli 21

Ezekieli 21:11-18