Ezekieli 20:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndinacicita cifukwa ca dzina langa, kuti lisadetsedwe pamaso pa amitundu amene anakhala pakati pao, amene pamaso pao ndinadzidziwitsa kwa iwo, pakuwaturutsa m'dziko la Aigupto.

Ezekieli 20

Ezekieli 20:1-19