Ezekieli 20:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati pfungo lokoma ndidzakulandirani pakukuturutsani mwa mitundu ya anthu, ndipo ndidzakusonkhanitsani kukucotsani m'maiko munabalalikiramo, ndipo ndidzazindikirika Woyera mwa inu pamaso pa amitundu.

Ezekieli 20

Ezekieli 20:40-47