Ezekieli 20:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakuturutsani mwa mitundu ya anthu, ndi kukusonkhanitsani m'maiko munabalalikamo ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi ukali wotsanulidwa.

Ezekieli 20

Ezekieli 20:28-42