Ezekieli 20:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace uziti kwa nyumba ya Israyeli, Atero Ambuye Yehova, Mudzidetsa kodi monga umo anacitira makolo anu? mucita cigololo kodi kutsata zonyansa zao?

Ezekieli 20

Ezekieli 20:24-39