Ezekieli 20:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndinabweza dzanja langa ndi kucicita, cifukwa ca dzina langa; kuti lisaipsidwe pamaso pa amitundu, amene ndinawaturutsa pamaso pao. Ndinawakwezeranso dzanja langa m'cipululu,

Ezekieli 20

Ezekieli 20:16-32