Ezekieli 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwe, wobadwa ndi munthu, tamvera ici ndirikunena nawe; usakhale iwewopanduka, ngati nyumba ija yopanduka; tsegula pakamwa pako, nudye comwe ndikupatsa.

Ezekieli 2

Ezekieli 2:1-10