Ezekieli 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwowa, ngakhale akamva kapena akaleka kumva, (pakuti ndiwo nyumba yopanduka,) koma adzadziwa kuti panali mneneri pakati pao.

Ezekieli 2

Ezekieli 2:1-10