Ezekieli 18:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

wosasautsa munthu ali yense, koma wambwezera wangongole cigwiriro cace, wosatenga zofunkha, anampatsa wanjala cakudya cace, nabveka wamarisece ndi cobvala,

Ezekieli 18

Ezekieli 18:3-12