Ezekieli 18:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tayani, ndi kudzicotsera zolakwa zanu zonse zimene munalakwa nazo, ndi kudzifunira mtima watsopano, ndi mzimu watsopano; pakuti mudzaferanji inu, nyumba ya Israyeli?

Ezekieli 18

Ezekieli 18:25-32