Ezekieli 18:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma nyumba ya Israyeli imanena, Njira ya Ambuye njosayenera, Inu, nyumba ya Israyeli, kodi njira zanga nzosayenera? njira zanu si ndizo zosayenera?

Ezekieli 18

Ezekieli 18:20-32