Ezekieli 18:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

naletsa dzanja lace pa wozunzika, wosalandira phindu kapena coonjezerapo, wocita maweruzo anga, nayenda m'malemba anga; uyu sadzafera mphulupulu ya atate wace, adzakhala ndi moyo ndithu.

Ezekieli 18

Ezekieli 18:15-25