Ezekieli 17:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Ambuye Yehova, Ndidzatenganso nsonga ya mkungudza wautali ndi kulika; ndidzabudula nsonga yosomphoka'ya nthambi zace zanthete, ndi kuioka pa phiri lalitali lothubvuka;

Ezekieli 17

Ezekieli 17:13-24