Ezekieli 17:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uziti tsono kwa nyumba ya mpandukoyi, Simudziwa kodi izi nciani? Uziti, Taonani mfumu ya ku Babulo inadza ku Yerusalemu, nitenga mfumu yace ndi akalonga ace, nibwera nao kuti iye ku Babulo;

Ezekieli 17

Ezekieli 17:7-18