Ezekieli 16:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinakucurukitsa ngati mphundu za kumunda; ndipo unathululuka ndi kukula kufikira wakongola nkhope, maere ako anamera, ndi tsitsi lako linamera; koma unali wamarisece ndi wausiwa.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:1-8