Ezekieli 16:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, mphulupulu ya mng'onowako Sodomu ndi iye, kudzikuza, kucuruka kwa cakudya, ndi kupumula kwa mtambasali, anali nako iye ndi ana ace; ndipo sanalimbitsa dzanja la wosauka ndi wosowa.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:44-54