Ezekieli 16:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mkulu wako ndiye Samariya, wokhala ku dzanja lako lamanzere, iye ndi ana ace akazi; ndi mng'ono wako wokhala ku dzanja lako lamanja ndiye Sodomu ndi ana ace akazi.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:44-56