Ezekieli 16:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mwemo ukali wanga udzakhuta nawe, ndi nsanje yanga idzakucokera, ndipo ndidzakhala cete wosakwiyanso.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:34-52