Ezekieli 16:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo za kubadwa kwako, tsiku lobadwa iwe sanadula ncofu yako, sanakuyeretsa ndi kukusambitsa ndi madzi, sanakuthira mcere konse, kapena kukukulunga m'nsaru ai.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:1-12