Ezekieli 16:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzaweruza mlandu wako, monga aweruza akazi acigololo ndi okhetsa mwazi; ndipo ndidzakutengera mwazi wa ukali ndi wa nsanje.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:32-44