Ezekieli 16:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Ambuye Yehova, Popeza ndalama zako zamwazika, nubvundukuka umarisece wako mwa cigololo cako ndi mabwenzi ako, ndi cifukwa ca mafano onse a zonyansa zako, ndi mwazi wa ana ako umene unawa patsa;

Ezekieli 16

Ezekieli 16:31-42