Ezekieli 16:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu amaninkha akazi onse acigololo mphatso, koma iwe umaninkha mabwenzi ako onse mphatso zako ndi kuwalipira, kuti akudzere kucokera ku mbali zonse, kuti acite nawe cigololo.

Ezekieli 16

Ezekieli 16:25-35