Ezekieli 14:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzakusangalatsani pamene muona njira yao, ndi zocita zao; ndipo mudzadziwa kuti sindinazicita kopanda cifukwa zonse ndinazicita momwemo, ati Ambuye Yehova.

Ezekieli 14

Ezekieli 14:20-23