Ezekieli 14:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cinkana anthu omwewo atatu akadakhala m'mwemo, Pali Ine, ati Ambuye Yehova, sakadapulumutsa ana amuna kapena akazi; iwo akadapulumuka okha; koma dziko likadakhala lacipululu.

Ezekieli 14

Ezekieli 14:8-23