Ezekieli 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti nyumba ya Israyeli isasocerenso kusatsata Ine, kapena kudzidetsanso ndi zolakwa zao zonse; koma kuti akhale anthu anga, ndipo ndikhale Ine Mulungu wao, ati Ambuye Yehova.

Ezekieli 14

Ezekieli 14:7-18