Ezekieli 14:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo anafika kwa ine akulu ena a Israyeli nakhala pansi pamaso panga.

2. Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti,

Ezekieli 14