Ezekieli 13:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mundidetsa mwa anthu anga kulandirapo barele wodzala manja, ndi zidutsu za mkate, kuipha miyoyo yosayenera kufa, ndi kusunga miyoyo yosayenera kukhala ndi moyo, ndi kunena mabodza kwa anthu anga omvera bodza.

Ezekieli 13

Ezekieli 13:10-20