Ezekieli 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza, inde popeza asokeretsa anthu anga, ndi kuti, Mtendere, pokhala palibe mtendere; ndipo anthu akamanga linga, aneneriwo alimata ndi dothi losapondeka;

Ezekieli 13

Ezekieli 13:1-19