Ezekieli 12:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace unene nao, Atero Yehova Mulungu, Ndidzaleketsa mwambi uwu, ndipo sadzauchulanso mwambi m'Israyeli; koma unene nao, Masiku ayandikira, nadzacitika masomphenya ali onse.

Ezekieli 12

Ezekieli 12:15-28