Ezekieli 12:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, ukhala pakati pa nyumba yampanduko, yokhala nao maso akuonera, koma osaona; ndi makutu akumvera, koma osamva; pakuti iwo ndiwo nyumba yampanduko.

Ezekieli 12

Ezekieli 12:1-6