Ezekieli 11:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mzimu wa Yehova unandigwera, ndipo ananti kwa ine, Nena, Atero Yehova, Mwatero nyumba ya Israyeli, pakuti ndidziwa zimene zimalowa m'mtima mwanu.

Ezekieli 11

Ezekieli 11:1-14