Ezekieli 11:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mzimu unandikweza, nufika nane m'masomphenya mwa mzimu wa Mulungu ku dziko la Akasidi, kwa andendewo. M'mwemo masomphenya ndidawaona anandicokera, nakwera.

Ezekieli 11

Ezekieli 11:21-25