Ezekieli 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzawapatsa mtima umodzi, ndi kuika mzimu watsopano m'kati mwao; ndipo ndidzawacotsera mtima wamwala m'thupi mwao, ndi kuwapatsa mtima wamnofu;

Ezekieli 11

Ezekieli 11:17-24