Ezekieli 10:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo thupi lao lonse, ndi misana yao, ndi manja ao, ndi mapiko ao, ndi njinga zomwe, zinadzala ndi maso pozungulira pao, zingakhale njingazi anai aja anali nazo.

Ezekieli 10

Ezekieli 10:8-18