Ezekieli 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mapazi ao anali mapazi oongoka, ndi ku mapazi ao kunanga kuphazi kwa mwana wa ng'ombe; ndipo ananyezimira ngati mawalidwe a mkuwa wowalitsidwa.

Ezekieli 1

Ezekieli 1:1-11