Ezekieli 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuli konse mzimu ukuti umuke, zinamuka komwe mzimu ukuti umuke; ndi njingazi zinanyamuka pambali pa izo; pakuti mzimu wa zamoyozo unali m'njingazo.

Ezekieli 1

Ezekieli 1:15-25