Ezara 8:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukhale maso ndi kuzisunga mpaka muziyesera pamaso pa akulu a ansembe ndi Alevi, ndi akulu a nyumba za makolo a Israyeli ku Yerusalemu, m'zipinda za nyumba ya Yehova.

Ezara 8

Ezara 8:19-33