Ezara 8:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinapatula akulu a ansembe khumi ndi awiri, ndiwo Serebiya, Hasabiya, ndi abale ao khumi pamodzi nao,

Ezara 8

Ezara 8:14-32