Ezara 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo aneneri, Hagai mneneriyo, ndi Zekariya mwana wa Ido, ananenera kwa Ayuda okhala m'Yuda ndi m'Yerusalemu; m'dzina la Mulungu wa Israyeli ananenera kwa iwo.

Ezara 5

Ezara 5:1-11