Ezara 4:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinalamulira anthu, nafunafuna, napeza kuti mudzi uwu unaukira mafumu kuyambira kale lomwe ndi kuti akacitamo mpanduko ndi kudziyendera.

Ezara 4

Ezara 4:18-24