Ezara 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adziwe mfumu kuti, Ayuda adakwerawo ocokera kwanu atifikira ife ku Yerusalemu, alikumanga mudzi uja wopanduka ndi woipa, alikutsiriza malinga ace, nalumikiza maziko ace.

Ezara 4

Ezara 4:8-18