Ezara 2:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana a odikira: ana a Sabumu, ana a Ateri, ana a Talimoni, ana a Akubu, ana a Hatita, ana a Sobai, onse pamodzi ndiwo zana limodzi mphambu makumi atatu kudza asanu ndi anai.

Ezara 2

Ezara 2:35-46